Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w02 12/15 tsamba 31
  • Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2002

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2002
  • Nsanja ya Olonda—2002
  • Timitu
  • BAIBULO
  • MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
  • MBIRI YA MOYO WANGA
  • MBONI ZA YEHOVA
  • MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
  • NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA
  • NKHANI ZOSIYANASIYANA
  • OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA
  • YEHOVA
  • YESU KRISTU
Nsanja ya Olonda—2002
w02 12/15 tsamba 31

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2002

Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo

BAIBULO

Baibulo la Septuagint, 9/15

Kuvutikira Kuti Likhale M’Chigiriki Chamakono, 11/15

Zomwe Mfumu Henry VIII Inachita Zokhudza Baibulo, 1/1

MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA

Anthu Ambirimbiri Adzasokeretsedwa pa Chiyeso Chomaliza? (Chiv 20:8), 12/1

Bwalo la Kachisi Kumene “Khamu Lalikulu” Limatumikira (Chiv 7:15), 5/1

Kodi Abele Anadziŵa Kuti Nyama Ndi Imene Inafunika Popereka Nsembe? 8/1

Kodi Chifundo cha Yehova Chimachepetsa Chilungamo Chake? 3/1

Kodi Kupanda Ungwiro kwa Mariya Kunaipitsa Yesu? 3/15

Kodi Munthu Akawinda kwa Mulungu Sangasinthe Zivute Zitani? 11/15

Kuchuluka kwa Ana a Jese (1Sa 16:10, 11; 1Mbiri 2:13-15), 9/15

Kugula Nyumba ya Chipembedzo N’kukhala Nyumba ya Ufumu? 10/15

Kukamba Nkhani pa Maliro a Munthu Wodzipha Yekha? 6/15

Kukhala Nawo pa Mwambo wa Maliro Kapena Ukwati M’tchalitchi? 5/15

Kumiza Thupi Lonse Ngakhale Munthu wa Chilema Chachikulu? 6/1

Kupemphera kwa Mulungu Popanda Kunena Mawu Akuti “M’dzina la Yesu,” 4/15

Kuphunzitsa Ana Ngati Kholo Lina Ndi la Mboni za Yehova Ndipo Linalo si Mboni, 8/15

Lusifara (Yes 14:12, KJ), 9/15

N’kulakwa Kutchova Njuga Ngati Ndalama Zobetcherana N’zochepa? 11/1

Nthaŵi Ziti Pamene Mkazi Wachikristu Ayenera Kuvala Chophimba Kumutu? 7/15

Tanthauzo la Mawu Akuti “Simunakana Kufikira Mwazi” (Aheb 12:4), 2/15

Ukwati wa Pachibale, 2/1

MBIRI YA MOYO WANGA

Dziko Limene Anatitumiza Kukachita Umishonale Linadzakhala Kwathu (D. Waldron), 12/1

Kuphunzitsa Ana Athu Kukonda Yehova (W. Matzen), 5/1

Kupindula Chifukwa Chodzipereka Kutumikira Mulungu (W. Aihinoria), 6/1

Kutumikira ndi Mzimu Wodzimana (D. Rendell), 3/1

Mwayi Wapadera Wogwira Nawo Ntchito Yofutukula Nkhondo Itatha (F. Hoffmann), 10/1

Ndakalamba Ndipo Ndakhutira ndi Zaka za Moyo Wanga (M. Smith), 8/1

“Sindingasinthe Kanthu!” (G. Allen), 9/1

Sitinasiye Ntchito Yomwe Tinapatsidwa (H. Bruder), 11/1

Ubale Wapadziko Lonse Wandilimbikitsa (T. Kangale), 7/1

Yehova Anatiphunzitsa Kupirira (A. Apostolidis), 2/1

Yehova Wapereka “Mphamvu Yoposa Yachibadwa” (H. Marks), 1/1

MBONI ZA YEHOVA

Achinyamata Ofanana ndi Mame Opatsa Mpumulo, 9/15

Achinyamata Okonda Choonadi, 10/1

Anthu Amakono Ofera Chikhulupiriro (Sweden), 2/1

Anthu Othandiza Kulambira Koona (zopereka), 11/1

Apasitala Omwe Anayamikira Zimene Russell Analemba, 4/15

“Chifukwa Chomwe Ndikukubwezerani Ndalama Zanu,” 8/15

‘Chikondi Chathu Chalimbikitsidwa’ (Phiri Lophulika la ku Japan), 3/1

Kodi Kusungabe Chikumbumtima Chabwino Tingakuvutikire Mpaka Pati? 2/15

Kuphunzira Kuŵerenga (Chilumba cha Solomon), 8/15

Mapiri a ku Philippines, 4/15

Mapulogalamu Omaliza Maphunziro a Gileadi, 6/15, 12/15

Mayiko a ku Balkan (Baibulo la New World Translation), 10/15

Misonkhano, 3/15

Misonkhano Yachigawo Yakuti “Aphunzitsi a Mawu a Mulungu,” 1/15

Misonkhano ya Mayiko mu 2003, 7/1

Mmene Anthu Akuwonjezekera Pakufunika Nyumba Zina (Nyumba za Ufumu), 5/15

Mmene Mwana Wamwamuna Anathandizira Bambo Wake, 5/1

Msonkhano Wapachaka cha 2001, 4/1

Nawonso Ali ndi Nzeru Zawo (zopereka za ana), 2/1

Ntchito Imene Imalimbikitsa Makhalidwe Abwino (Mozambique), 11/15

Ntchito Zabwino Zimalemekeza Mulungu (Italy), 1/15

Nyumba ya Ufumu Ilandira Mendulo Yaulemu (Finland), 10/1

Pa Tebulo la Mmalinyero Wamkulu (R. G. Smith), 12/1

“Tichitire Onse Chokoma,” 7/15

Wina Aliyense Ndi Wolandiridwa pa Nyumba ya Ufumu, 11/1

MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU

Akulu​—Phunzitsani Ena, 1/1

Bzalani Chilungamo, Kololani Kukoma Mtima (Miy 11), 7/15

Chikondi M’banja, 12/15

“Chipulumutso N’cha Yehova” (mapulogalamu olimbikitsa mzimu wokonda dziko), 9/15

Chisoni, 4/15

“Khala Ukudziphunzitsa,” 10/1

‘Khululukiranani,’ 9/1

Kodi Mayesero Tiziwaona Bwanji? 9/1

Kodi Mumaphunzitsa Zogwira Mtima? 7/1

Kodi Yehova Amadalitsa Liti Khama la Munthu? 8/1

Kukhulupirika, 8/15

‘Kulalikira Mawu’ Kumadzetsa Mpumulo, 1/15

Kulera Ana M’dziko Lachilendo, 10/15

Kuongoka Mtima Kumatsogolera Olungama (Miy 11), 5/15

Kupepesa, 11/1

Kusangalatsa Yehova Ndi Masiku a Moyo Wathu, 11/15

Kusonkhana Pamodzi, 11/15

Kusungulumwa, 3/15

Kuyamikira, 11/1

Kuyenda M’njira za Yehova, 7/1

Limbitsani Manja Anu, 12/1

Luso la Kulingalira, 8/15

Malo Obisalirako Mphepo, 2/15

Mulungu Amalandira Anthu a Mitundu Yonse, 4/1

Nsanje, 10/15

Ukhondo, 2/1

“Wetani Gulu la Mulungu,” 11/15

Zinsinsi, 6/15

NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA

“Adzayandikira kwa Inu,” 12/15

Akristu Amafunika Kuthandizana, 11/15

Akristu Amalambira Mumzimu ndi M’choonadi, 7/15

Akristu Onse Oona Amalalikira, 1/1

Akristu Osalowerera M’zinthu za Dziko M’masiku Otsiriza, 11/1

Amayendabe M’choonadi, 7/15

Anatiyeretsa Kuti Tichite Ntchito Zokoma, 6/1

Anthu Okhulupirika Analimbana ndi Minga M’matupi Awo, 2/15

Gonjerani Mokhulupirika Ulamuliro Umene Mulungu Waika, 8/1

“Kanizani Mdyerekezi,” 10/15

Khalani Omvera Pamene Mapeto Akuyandikira, 10/1

Kodi Choonadi N’chamtengo Wapatali Motani kwa Inu? 3/1

Kodi Muli Nawo M’gulu la Anthu Amene Mulungu Amawakonda? 2/1

Kodi Mwalandira “Mzimu wa Choonadi”? 2/1

Kodi Ndani Adzapulumuka Tsiku la Yehova? 5/1

Kodi Utsogoleri wa Kristu Mumauonadi Kukhala Weniweni? 3/15

Komerani Mtima Anthu Osowa Thandizo, 5/15

Kondani Phunziro Laumwini la Mawu a Mulungu, 12/1

Kondwerani ndi Chilungamo cha Yehova, 6/1

“Kopanda Fanizo Sanalankhula Kanthu kwa Iwo,” 9/1

Kristu Amatsogolera Mpingo Wake, 3/15

Kuchita Zimene Mulungu Amafuna Kumalemekeza Yehova, 5/1

Kulimbana ndi “Munga M’thupi,” 2/15

Kulimbikitsidwa ndi “Zazikulu za Mulungu,” 8/1

Kupindula ndi Kukoma Mtima kwa Yehova, 5/15

Kuunika kwa Mulungu Kumachotsa Mdima! 3/1

Malamulo a Mulungu Amatipindulitsa, 4/15

“Mayendedwe Anu mwa Amitundu Akhale Okoma,” 11/1

N’chifukwa Chiyani Tifunika Kubatizidwa? 4/1

“Ndakupatsani Inu Chitsanzo,” 8/15

‘Nditsatireni Ine Nthaŵi Zonse,’ 8/15

“Nthaŵi Yonse Palibe Munthu Analankhula Chotero,” 9/1

Okonzeka Mokwanira Kukhala Aphunzitsi a Mawu a Mulungu, 2/15

Onjezerani Kudzipereka kwa Mulungu pa Chipiriro Chanu, 7/15

Phindu la Uthenga Wabwino, 1/1

Phunzirani ndi Kuphunzitsa Ena Makhalidwe Abwino Achikristu, 6/15

Phunziro Laumwini Limene Limatikonzekeretsa Monga Aphunzitsi, 12/1

Pitirizani Kuchita Zabwino, 1/15

Pitirizani Kuchita Zimene Mwaphunzira, 9/15

Pitirizani Kutumikira ndi Mtima Umodzi, 11/15

Pitirizani Kutumikira Yehova ndi Mtima Wokhazikika, 4/1

‘Samaliranidi,’ 9/15

Tsanzirani Chitsanzo cha Mfumu, 6/15

Tsanzirani Mphunzitsi Wamkulu, 9/1

Ulemerero wa Yehova Umawalira Anthu Ake, 7/1

“Yandikirani kwa Mulungu,” 12/15

Yehova Amadalitsa ndi Kuteteza Anthu Omvera, 10/1

Yehova Amadana ndi Chinyengo, 5/1

Yehova Amakometsera Anthu Ake ndi Kuunika, 7/1

Yehova Amakusamalirani, 10/15

Yehova Ndiye Chitsanzo Chachikulu Pankhani Yosonyeza Ubwino, 1/15

Yendani Motsatira Mfundo za Makhalidwe Abwino za Mulungu, 4/15

NKHANI ZOSIYANASIYANA

Anthu Awiri a Pachibale Amene Anali ndi Mitima Yosiyana (Kaini ndi Abele), 1/15

Anthu Okhala Nawo Pafupi, 9/1

“Anthu Oyera Mtima,” 9/15

“Anzeru a Kum’maŵa,” 12/15

Awadensi, 3/15

Chilimbikitso Panthawi ya Mavuto, 10/1

Chimene Tingaphunzirepo pa Mbiri ya Aroma (maseŵera omenyana), 6/15

Chinthu Choposa Chuma cha Aigupto (Mose), 6/15

Dziko Lakale Linawonongedwa (Chigumula), 3/1

Guwa la Nsembe la Mulungu Wosadziwika, 7/15

Imfa, 6/1

Khulupirirani Mulungu Amene Ndi Weniweni, 1/15

Kodi Chikhulupiriro Chimafuna Kuganiza? 4/1

Kodi Moyo Wabwino Mungaupeze Kuti? 4/15

Kodi Muli ndi Vuto Ndinu Kapena Chibadwa Chanu? 6/1

Kodi Muyenera Kukhala Waphee Kapena Wamphwayi? 10/1

Kodi Ndalama Zoyendetsera Chipembedzo Zizipezedwa Bwanji? 12/1

Kodi Timafunikira Malo Olambiriramo? 11/15

Kodi Zidzathekadi Kuti Anthu Onse Akhale Ofanana? 1/1

“Konzekerani Kumva Kuwawa,” 3/1

Kukhulupirika kwa Ndani? 8/15

Kulumala Konse Kudzatha, 5/1

Kuumitsa Mtembo, 3/15

Mafano Azithunzi, 7/1

Malodza, 8/1

Masewero a Yoga, 8/1

Mavuto a Anthu, 6/15

Mfundo za Chikhalidwe za Mulungu Zingapindulitse, 2/15

“Mkazi Waulemu“ (Rute), 6/15

Moto wa Helo, 7/15

Mtengo “Wolira” ndi “Misozi” Yake, 1/15

Mudzi Wokhala Pamwamba pa Phiri, 2/1

Musanyengedwe, 7/1

Nikodemo, 2/1

Safani ndi Banja Lake, 12/15

Satana​—Kodi Ndi Wongopeka Kapena Ndi Munthu Woipa Yemwe Alipodi? 10/15

Tchalitchi Ndiponso Boma Mumzinda wa Bezantiyamu, 2/15

Tertullian, 5/15

Ubatizo wa Clovis, 3/1

Utsogoleri Wabwino, 3/15

Yoswa, 12/1

Zikhulupiriro Zopeka Zokhudza Imfa, 6/1

Zomwe Tingaphunzire ku Mbalame Yotchedwa Dokowe, 8/1

OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA

2/1, 4/1, 6/1, 8/1, 10/1, 11/1

YEHOVA

Khulupirirani Yehova, Amene Ndi Weniweni, 1/15

Kodi Mulungu Ndani? 5/15

Zilembo Zinayi Zoimira Dzina la Mulungu mu Baibulo la Septuagint, 6/1

YESU KRISTU

Kubadwa kwa Yesu, 12/15

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena