Zamkatimu
March 15, 2008
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MLUNGU WA:
April 21-27, 2008
Khalani Ololera Koma Mosapitirira Malire
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 8, 177
April 28, 2008–May 4, 2008
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 117, 89
May 5-11, 2008
Yehova Amamva Kulira Kwathu Ndipo Amatithandiza
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 58, 135
May 12-18, 2008
“Kodi Wanzeru ndi Womvetsa Zinthu Ndani Pakati pa Inu?”
TSAMBA 21
NYIMBO ZOIMBA: 106, 51
May 19-25, 2008
Kodi Mumaona Anthu Mmene Yehova Amawaonera?
TSAMBA 25
NYIMBO ZOIMBA: 127, 213
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11
Mosiyana ndi zimene anthu ambiri amaganiza, pali zifukwa zabwino zimene Akhristu afunikira kukhala ololera. Kodi zifukwazo ndi zotani? Ndipo kodi muyenera kuchita chiyani kuti mukhale ololera muukwati wanu?
Nkhani Zophunzira 3 MASAMBA 12-16
N’chifukwa chiyani tili ndi chikhulupiriro chakuti Yehova amamva kulira kwathu ndipo amatithandiza? Nkhani imeneyi ikuyankha funsoli ndipo ikusonyeza mmene tingapezere mphamvu kuti tipirire mayesero.
Nkhani Zophunzira 4, 5 MASAMBA 21-29
Nkhani ziwirizi zitithandiza kuti tiziona anthu moyenera ndi kupewa chizolowezi chimene ambiri ali nacho chokonda kuweruza anzawo. Ndipo tiona kusiyana pakati pa munthu wanzeru ndi wopanda nzeru.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Kufalitsa Uthenga Wabwino M’mapiri a Andes
TSAMBA 16
TSAMBA 19
Mawu a Yehova Ndi Amoyo—Mfundo Zazikulu za M’buku la Luka
TSAMBA 30