Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w08 5/15 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Nsanja ya Olonda—2008
  • Timitu
  • NKHANI ZOPHUNZIRA MLUNGU WA:
  • Cholinga cha Nkhani Zophunzira
  • M’MAGAZINI INO MULINSO:
Nsanja ya Olonda—2008
w08 5/15 tsamba 1-2

Zamkatimu

May 15, 2008

Magazini Yophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA MLUNGU WA:

June 30, 2008–July 6, 2008

Kodi Tizikhala Bwanji ndi Anzathu?

TSAMBA 3

NYIMBO ZOIMBA: 35, 62

July 7-13, 2008

Pitirizani Kuchita Zabwino

TSAMBA 7

NYIMBO ZOIMBA: 95, 145

July 14-20, 2008

Chipulumutso Kudzera mu Ufumu wa Mulungu Chayandikira!

TSAMBA 12

NYIMBO ZOIMBA: 181, 130

July 21-27, 2008

Sankhani Kutumikira Yehova Mudakali Achinyamata

TSAMBA 17

NYIMBO ZOIMBA: 157, 221

July 28, 2008–August 3, 2008

Pitani Patsogolo Mwauzimu Potsanzira Paulo

TSAMBA 21

NYIMBO ZOIMBA: 123, 129

Cholinga cha Nkhani Zophunzira

Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11

Paulaliki wake wotchuka wapaphiri, Yesu anatsindika kufunika kokhala ofatsa, achifundo ndi odzetsa mtendere. Analimbikitsa otsatira ake ‘kuonetsa kuwala kwawo,’ ndipo iye anafotokoza zimene tiyenera kuchitira adani athu ndiponso anthu ena.

Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 12-16

Dziwani mmene mungafotokozere chifukwa chimene tikufunikira kwambiri chipulumutso panopa kuposa kale lonse. Onani chifukwa chake Yehova ali Mpulumutsi Wamkulu ndi mmene mungasonyezere ena kuti Ufumu wa Mulungu upulumutsa anthu posachedwapa.

Nkhani Zophunzira 4, 5 MASAMBA 17-25

N’chifukwa chiyani achinyamata ayenera kutumikira Mulungu? Kodi iwo zingawayendere bwino atadzipereka kwa Yehova, ngakhale anthu aziwaona bwanji? Kodi iwo angachite utumiki wotani? Kodi chitsanzo cha mtumwi Paulo chingatithandize bwanji tonse mumpingo kupita patsogolo mwauzimu? Nkhani ziwirizi zikuyankha mafunso ofunika kwambiri amenewa.

M’MAGAZINI INO MULINSO:

Khalani ‘Oyera Poopa Mulungu’

TSAMBA 26

Mmene Bungwe Lolamulira Limayendetsera Ntchito Zake

TSAMBA 29

Mawu a Yehova Ndi Amoyo​—Mfundo Zazikulu za M’buku la Machitidwe

TSAMBA 30

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena