Zamkatimu
June 15, 2008
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MLUNGU WA:
August 4-10, 2008
Zinthu Zimene Tiyenera Kuthawa
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 139, 146
August 11-17, 2008
Makhalidwe Amene Tiyenera Kutsatira
TSAMBA 11
NYIMBO ZOIMBA: 42, 54
August 18-24, 2008
TSAMBA 18
NYIMBO ZOIMBA: 47, 2
August 25-31, 2008
Musasiye ‘Chikondi Chimene Munali Nacho Poyamba’
TSAMBA 22
NYIMBO ZOIMBA: 201, 132
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 7-15
Timakhulupirira kuti Mulungu amatikonda. Umboni wa zimenezi ndi wakuti iye watiuza zinthu zinayi zimene Akhristufe tiyenera kuzithawa. Kodi zinthu zimenezi ndi ziti, ndipo tingazithawe bwanji? Komanso, Baibulo limatchula zinthu 7 zimene tiyenera kuzitsatira. Kodi zinthu zimenezi ndi ziti, ndipo tingazitsatire bwanji?
Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 18-22
Mzimu wofuna kudziimira pawekha ndi wofala m’dzikoli. Ndiyeno, kodi tingatani kuti tizilemekeza ulamuliro, makamaka wa Yehova? Nkhani imeneyi itithandiza kudziwa mmene tingachitire zimenezi, komanso mmene tingapewere mzimu wofuna kudziimira pawekha umene Satana amalimbikitsa.
Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 22-26
Nkhani yophunzira imeneyi itithandiza kuganizira zimene zinatichititsa kuyamba choonadi ndiponso kukonda Yehova. Ikupereka malangizo a zimene munthu angachite kuti ayambe kukondanso Yehova ndi choonadi, ngati chikondicho chakhala chikuzirala.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Tingakhale Amphamvu Ngakhale Tili ndi Zofooka
TSAMBA 3
Kodi Ndinu Wokonzeka Kufotokoza za Chikhulupiriro Chanu?
TSAMBA 16
Kodi Yesu Anali Kunena za Moto wa Helo?
TSAMBA 27
TSAMBA 28
Mawu a Yehova Ndi Amoyo Mfundo Zazikulu za M’kalata ya Aroma
TSAMBA 29
TSAMBA 32