Zamkatimu
July 15, 2008
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MLUNGU WA:
September 1-7, 2008
N’chifukwa Chiyani Utumiki wa ku Nyumba ndi Nyumba Uli Wofunika Kwambiri Masiku Ano?
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 32, 162
September 8-14, 2008
Kodi Tingatani ndi Mavuto Amene Timakumana Nawo Muutumiki wa ku Nyumba ndi Nyumba?
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 53, 92
September 15-21, 2008
‘Mulungu Ndi Amene Amakulitsa’!
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 133, 211
September 22-28, 2008
TSAMBA 17
NYIMBO ZOIMBA: 148, 192
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11
Mboni za Yehova zimadziwika padziko lonse lapansi chifukwa cha utumiki wawo wa ku nyumba ndi nyumba. Nkhani ziwirizi zikufotokoza chifukwa chake timagwiritsa ntchito kwambiri njira yolalikirira imeneyi, ndiponso mmene tingachitire ndi mavuto amene timakumana nawo polalikira khomo ndi khomo.
Nkhani Zophunzira 3, 4 MASAMBA 12-21
Nkhani zimenezi zikufotokoza mafanizo a Yesu asanu, olimbitsa chikhulupiriro chathu. Mfundo zina zimene zafotokozedwa mu nkhanizi ndi zatsopano. Nkhanizi zitithandiza kumvetsa mphamvu ya mzimu wa Mulungu, pamene tiphunzire mmene mafanizo asanuwa akusonyezera mmene ntchito yolalikira za Ufumu ikukulira m’njira zosiyanasiyana.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Sitinachite Mantha, Yehova Anali Nafe
TSAMBA 22
Mawu a Yehova Ndi Amoyo—Mfundo Zazikulu za M’makalata a ku Korinto
TSAMBA 26
Musadzipanikize, Ndipo Mudzakhala Achimwemwe
TSAMBA 29