Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w08 8/15 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Nsanja ya Olonda—2008
  • Timitu
  • NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
  • Cholinga Cha Nkhani Zophunzira
  • M’MAGAZINI INO MULINSO:
Nsanja ya Olonda—2008
w08 8/15 tsamba 1-2

Zamkatimu

August 15, 2008

Magazini Yophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:

September 29, 2008–​October 5, 2008

Yehova Sataya Anthu Ake Okhulupirika

TSAMBA 3

NYIMBO ZOIMBA: 114, 223

October 6-12, 2008

Khalani Okhulupirika ndi Mtima Wonse

TSAMBA 7

NYIMBO ZOIMBA: 38, 8

October 13-19, 2008

Lemekezani Yehova mwa Kusonyeza Ulemu

TSAMBA 12

NYIMBO ZOIMBA: 48, 136

October 20-26, 2008

Yehova Amasamalira Mwachikondi Atumiki Ake Okalamba

TSAMBA 17

NYIMBO ZOIMBA: 58, 216

October 27, 2008–November 2, 2008

Kodi Mumalankhula Bwino “Chinenero Choyera”?

TSAMBA 21

NYIMBO ZOIMBA: 78, 169

Cholinga Cha Nkhani Zophunzira

Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11

Zimene zinachitika panthawi imene mafuko 12 a Isiraeli anagawidwa kukhala ufumu wa kumpoto ndi wa kumwera, zikutiphunzitsa kuti Yehova sataya anthu ake okhulupirika. Nkhanizi zikugogomezera kuti tifunika kukhala okhulupirika ndi mtima wonse panopa kuti tipewe mtima wokonda chuma kapena wodzikuza.

Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 12-16

Nkhaniyi ikutiphunzitsa zimene tiyenera kuchita pozindikira ukulu wa Mulungu. Ikufotokoza zimene tikuphunzira kwa Yesu pankhani yosonyeza anthu ulemu ndipo ikutiphunzitsanso mmene tingasonyezere ulemu.

Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 17-21

Phunzirani kuwaona Akhristu okalamba mmene Yehova amawaonera. Muonanso mmene Baibulo limatithandizira kuti tizilemekeza zimene akudziwa, mmene akumvera, ndiponso kuwathandiza kukhalabe achangu pazochita zachikhristu.

Nkhani Yophunzira 5 MASAMBA 21-25

Kudzera mwa mneneri wake Zefaniya, Yehova anati: “Ndidzapatsa mitundu ya anthu mlomo woyera [“chinenero choyera,” NW].” (Zef. 3:9) Muphunzira kuti “chinenero choyera” n’chiyani. Onani zimene mungachite kuti muzilankhula bwino chinenerochi. Onaninso mmene mungagwiritsire ntchito chinenero chapaderachi potamanda Yehova.

M’MAGAZINI INO MULINSO:

Mawu a Yehova Ndi Amoyo​—Mfundo Zazikulu za M’makalata Opita kwa Agalatiya, Aefeso, Afilipi, ndi Akolose

TSAMBA 26

Kodi Mukukumbukira?

TSAMBA 29

Amishonale Ali Ngati Dzombe

TSAMBA 30

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena