Zamkatimu
February 15, 2009
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
April 6-12, 2009
Zimene Yesu Anaphunzitsa Zimatithandiza Kukhala Osangalala
TSAMBA 6
NYIMBO ZOIMBA: 57, 36
April 13-19, 2009
Mungakhale ndi Khalidwe Labwino mwa Kutsatira Zimene Yesu Anaphunzitsa
TSAMBA 10
NYIMBO ZOIMBA: 106, 132
April 20-26, 2009
Kodi Mapemphero Anu Amagwirizana ndi Zimene Yesu Anaphunzitsa?
TSAMBA 15
NYIMBO ZOIMBA: 88, 161
April 27, 2009–May 3, 2009
“Amatsatira Mwanawankhosa” Nthawi Zonse
TSAMBA 24
NYIMBO ZOIMBA: 213, 53
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1-3 MASAMBA 6-19
Yesu atamaliza ulaliki wake wa pa phiri, ‘khamu la anthu linakhudzidwa moti anazizwa ndi kaphunzitsidwe kake.’ (Mat. 7:28) Onani chifukwa chake anthuwo anazizwa, komanso onani mmene mawu ake angakuthandizireni kukhala wosangalala, wakhalidwe labwino ndiponso kupemphera movomerezeka.
Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 24-28
“Kapolo wokhulupirika ndi wanzeru” waikidwa kuti ‘aziyang’anira zinthu zonse’ za Khristu. (Mat. 24:45-47) Nkhani imeneyi ikufotokoza zifukwa zimene tiyenera kukhulupirira kapoloyu ndiponso mmene tingachitire zimenezi.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Mawu a Yehova Ndi Amoyo—Mfundo Zazikulu za M’buku la Chivumbulutso—Gawo 2
TSAMBA 3
Kodi Muyenera Kuumirira Zokonda Zanu?
TSAMBA 19
Amishonale Analimbikitsidwa Kutsanzira Yeremiya
TSAMBA 22
Mwambo wa Maliro Achikhristu Umakhala Wolemekezeka, Wosadzionetsera Ndiponso Wokondweretsa Mulungu
TSAMBA 29