Zamkatimu
June 15, 2009
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
August 3-9, 2009
Khalani Achangu pa Nyumba ya Yehova
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 31, 118
August 10-16, 2009
Khalani “Achangu pa Ntchito Zabwino”
TSAMBA 11
NYIMBO ZOIMBA: 30, 181
August 17-23, 2009
Lankhulani Zoona kwa Mnansi Wanu
TSAMBA 16
NYIMBO ZOIMBA: 192, 170
August 24-30, 2009
Mdindo Wokhulupirika ndi Bungwe Lake Lolamulira
TSAMBA 20
NYIMBO ZOIMBA: 51, 114
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 7-15
Mafumu anayi a Yuda anachita zazikulu kwambiri pochirikiza kulambira koona. Kodi chitsanzo chawo chingatiphunzitse chiyani pa nkhani ya changu chathu potumikira Yehova? Nkhani ziwirizi n’zosangalatsa ndiponso zili ndi malangizo abwino zedi.
Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 16-20
Tsiku ndi tsiku pamachitika zinthu zomwe zingatichititse kuganiza kuti chidule n’kungonama basi. Apo ayi tingaone kuti tikanena zoona ndiye kuti sitinam’ganizire winawake, kapenanso tinganene dala zinthu zoti wina asazimvetse. N’chifukwa chiyani Akhristu oona ayenera kuyesetsa kuti asamachite zimenezi? Kodi n’chiyani chingakuthandizeni pa nkhani imeneyi?
Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 20-24
Anthu a Mulungu amalemekeza kwambiri gulu la kapolo wokhulupirika ndi wanzeru. Koma kodi pali mgwirizano wotani pakati pa gulu limeneli ndi Bungwe Lolamulira? Ndipo kodi Malemba amati Yehova amatipatsa bwanji chakudya chauzimu masiku ano? Komanso kodi tiyenera kuwaona motani anthu amene amadya zizindikiro za pa Chikumbutso? Nkhaniyi iyankha mafunso amenewa mwatsatanetsatane.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Kodi Ndingam’bwezere Chiyani Yehova?
TSAMBA 3
Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala ndi Umbeta
TSAMBA 25
TSAMBA 28
TSAMBA 32