Zamkatimu
July 15, 2009
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
August 31, 2009–September 6, 2009
Fufuzani Chuma Chimene ‘Chinabisidwa Mosamala mwa Iye’
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 121, 105
September 7-13, 2009
Mabanja Achikhristu, Tsatirani Chitsanzo cha Yesu
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 205, 158
September 14-20, 2009
Phunzitsani Mwachikondi Ngati Yesu
TSAMBA 15
NYIMBO ZOIMBA: 156, 215
September 21-27, 2009
Tsanzirani Yesu mwa Kulalikira Molimba Mtima
TSAMBA 19
NYIMBO ZOIMBA: 92, 148
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Yophunzira 1 MASAMBA 3-7
Yehova akupempha atumiki ake onse kufufuza chuma chamtengo wapatali chimene “chinabisidwa mosamala” mwa Khristu. Kodi chuma chimenechi n’chiyani? Kodi tingachipeze bwanji? Kodi phindu lake ndi lotani? Nkhani imeneyi itithandiza kupeza mayankho.
Nkhani Yophunzira 2 MASAMBA 7-11
Kungoyambira pamene anthu analengedwa, Yesu wakhala akusonyeza chidwi ndi anthu. Nkhani imeneyi ikufotokoza mmene ziphunzitso za Yesu ndi chitsanzo chimene anapereka ali padziko lapansi, zingatithandizire tonsefe kukhala ogwirizana m’banja.
Nkhani Yophunzira 3, 4 MASAMBA 15-23
Kodi n’chifukwa chiyani Yesu anali mphunzitsi wogwira mtima? Chifukwa chachikulu n’chakuti ankakonda Yehova, anthu ndiponso uthenga umene ankalalikira. Chikondi chinamulimbikitsa kulalikira molimba mtima ngakhale pa nthawi imene ankatsutsidwa. Nkhani zimenezi zifotokoza zimene tiyenera kuchita kuti titsanzire Yesu n’kukhala aphunzitsi achikondi ndi alaliki olimba mtima.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Kodi Mumatsatira “Njira Yopambana” ya Chikondi?
TSAMBA 12
Ndinayamba ‘Kukumbukira Mlengi Wanga’ Zaka 90 Zapitazo
TSAMBA 24
Kugwirizana Kumathandiza Kuti Banja Lizikula Mwauzimu
TSAMBA 28
Landirani Moyamikira Ndipo Perekani ndi Mtima Wonse
TSAMBA 29
Mbewu za Choonadi Zafika Kumadera Akutali
TSAMBA 32