Zamkatimu
September 15, 2009
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
October 26, 2009–November 1, 2009
Khalani ndi Maganizo a Khristu
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 62, 66
November 2-8, 2009
Khalani Omvera Ndiponso Olimba Mtima Ngati Khristu
TSAMBA 11
NYIMBO ZOIMBA: 8, 107
November 9-15, 2009
Chikondi cha Khristu Chimatilimbikitsa Kukonda Ena
TSAMBA 16
NYIMBO ZOIMBA: 89, 35
November 16-22, 2009
Maphunziro Ochokera kwa Mulungu Ndi Opambanadi
TSAMBA 21
NYIMBO ZOIMBA: 91, 59
November 23-29, 2009
Kodi Mumayamikira Zimene Yehova Wachita Kuti Akupulumutseni?
TSAMBA 25
NYIMBO ZOIMBA: 55, 153
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1-3 TSAMBA 7-20
Tikudziwa kuti Yesu anapereka chitsanzo kwa Akhristu m’njira zambiri. Nkhani izi zikufotokoza bwino maganizo a Yesu ndiponso zochita zake. Muona mmene chitsanzo chake chingakuthandizireni m’banja mwanu, mumpingo ndiponso polimbana ndi mavuto.
Nkhani Yophunzira 4 TSAMBA 21-25
Kodi mumayamikira kwambiri choonadi chimene mwaphunzira m’Mawu a Mulungu? Nkhani imeneyi itithandiza kuganizira madalitso amene tapeza chifukwa cha maphunziro ochokera kwa Mulungu. Ikufotokozanso madalitso amene timapeza tikadzimana zinthu zina chifukwa cha uthenga wabwino.
Nkhani Yophunzira 5 TSAMBA 25-29
Kodi Yehova wachita chiyani kuti atipulumutse ku uchimo ndi imfa? Kodi anadzimana chiyani kuti zimenezi zitheke? Kudziwa mayankho a mafunso amenewa, kungatithandize kukhala ndi mtima woyamikira ndiponso kungatilimbikitse kuti timusonyeze Yehova kuti timayamikira kwambiri chiyembekezo cha chipulumutso chimene Iye ndi Mwana wake atipatsa.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Kodi Chipembedzochi Ndi Changa Kapena cha Makolo Anga?
TSAMBA 3
TSAMBA 30