Zamkatimu
May 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
June 28, 2010–July 4, 2010
Amuna, Kodi Mumagonjera Khristu Monga Mutu Wanu?
TSAMBA 8
NYIMBO ZOIMBA: 5, 42
July 5-11, 2010
Akazi, N’chifukwa Chiyani Muyenera Kugonjera Amuna Monga Mutu?
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 3, 6
July 12-18, 2010
Abale, Feserani Mzimu Ndipo Yesetsani Kuti Muyenerere Udindo
TSAMBA 24
NYIMBO ZOIMBA: 45, 11
July 19-25, 2010
Musamvetse Chisoni Mzimu Woyera wa Yehova
TSAMBA 28
NYIMBO ZOIMBA: 38, 26
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 MASAMBA 8-17
Nkhani yophunzira yoyamba ikufotokoza chifukwa chake amuna afunika kugonjera Mutu wawo, yemwe ndi Khristu ndiponso kumutsanzira pochita zinthu ndi ena. Nkhani yachiwiri ikufotokoza mmene akazi achikhristu ayenera kuonera mawu akuti: “Mutu wa mkazi ndi mwamuna.”
NKHANI ZOPHUNZIRA 3, 4 MASAMBA 24-32
Masiku ano, anthu ambiri safuna kuchita zinthu modzimana pofuna kuthandiza ena. Nkhani yoyamba yakonzedwa n’cholinga chothandiza makamaka amuna obatizidwa kuti aone mmene akuchitira pa nkhani yodzimana ndiponso ngati ali ndi mtima wofuna kukhala atumiki othandiza kapena akulu. Nkhani yachiwiri ikufotokoza mmene tingapewere kumvetsa chisoni mzimu woyera wa Mulungu.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
Akhristu Oyambirira Ndiponso Milungu ya Aroma 3
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kulemekeza Okalamba? 6
Khalanibe Olimba Mwauzimu Mukamasamalira Wachibale Amene Akudwala 17
Mumzinda wa Harana Munkachitika Zinthu Zambiri 20
Mafunso Ochokera kwa Owerenga 21
Pitirizani Kuphunzitsa Luntha Lanu la Kuzindikira 22