Zamkatimu
September 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
October 25-31, 2010
Muzifunafuna Madalitso a Yehova ndi Mtima Wonse
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 1, 38
November 1-7, 2010
Akhristu Oona Amadziwika Chifukwa cha Kugwirizana
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 20, 53
November 8-14, 2010
Mgwirizano wa Akhristu Umalemekeza Mulungu
TSAMBA 16
NYIMBO ZOIMBA: 20, 25
November 15-21, 2010
“Mtsogoleri Wanu ndi Mmodzi, Khristu”
TSAMBA 21
NYIMBO ZOIMBA: 5, 25
November 22-28, 2010
Mtsogoleri Wathu Akuchita Zambiri Masiku Ano
TSAMBA 25
NYIMBO ZOIMBA: 6, 44
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI YOPHUNZIRA 1 MASAMBA 7-11
Atumiki a Mulungu amafuna madalitso a Yehova kuti akwanitse kutsatira mfundo zake zolungama. Koma kodi n’chiyani chimene ayenera kuyesetsa kuchita? Kodi mzimu woyera wa Yehova ungatithandize bwanji kulimbana ndi mavuto alionse amene timakumana nawo?
NKHANI ZOPHUNZIRA 2, 3 MASAMBA 12-20
Nkhani ziwirizi zisonyeza kuti zimakhala zabwino ndiponso zosangalatsa ngati abale akukhala limodzi mogwirizana. Tionanso mfundo zotsimikizira kuti ndi Yehova yekha amene angagwirizanitse mitundu yonse ya anthu. Kenako tikambirana zimene aliyense payekha angachite polimbikitsa mgwirizano mumpingo chifukwa izi zimalemekeza Mulungu.
NKHANI ZOPHUNZIRA 4, 5 MASAMBA 21-29
Nkhani ziwirizi zitithandiza kudziwa bwino Khristu monga Mfumu kumwamba ndiponso Wolamulira wathu amene akuchita zambiri masiku ano. Iye amaona bwinobwino zimene zikuchitika m’mipingo ya ophunzira ake masiku ano.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
Kutumikira pa Nthawi Imene Ntchito Yolalikira Yapita Patsogolo Kwambiri 3
Ntchito Yapadera ku Bulgaria Inali ndi Zotsatira Zabwino 30