Zamkatimu
May 1, 2011
Maulosi 6 A M’baibulo Amene Akukwaniritsidwa Masiku Ano
NKHANI ZOYAMBIRIRA
7 Ulosi Wachinayi: Kupanda Chikondi
8 Ulosi Wachisanu: Kuwononga Dziko
9 Ulosi Wa 6: Ntchito Yolalikira Imene Ikuchitika Padziko Lonse
10 Posachedwapa Zinthu Padzikoli Zikhala Bwino
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
11 Chinsinsi cha Banja Losangalala—Kodi Zinthu Zimasintha Bwanji M’banja Mukabadwa Mwana?
22 Zoti Achinyamata Achite—Muzipewa Kucheza Ndi Anthu a Makhalidwe Oipa
31 Yandikirani Mulungu—“Yehova Ndi M’busa Wanga”
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
18 Anthu Okonda Mtendere Akuyesetsa Kuti Anthu Asaipitse Mbiri Yawo
24 Moyo wa Anthu Akale—Ndalama
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
COVER: Earthquake and Disease: © William Daniels/Panos Pictures; Famine: © Paul Lowe/Panos Pictures; Oil fire: U.S. Coast Guard photo