Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w11 7/15 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Nsanja ya Olonda—2011
  • Timitu
  • NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
  • Cholinga cha Nkhani Zophunzira
  • M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
Nsanja ya Olonda—2011
w11 7/15 tsamba 1-2

Zamkatimu

July 15, 2011

Magazini Yophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:

August 29, 2011–September 4, 2011

Kodi Mukutsatira Malangizo Achikondi a Yehova?

TSAMBA 10

NYIMBO ZOIMBA: 26, 3

September 5-11, 2011

Kodi Mukutsatira Machenjezo a Yehova Omveka Bwino?

TSAMBA 15

NYIMBO ZOIMBA: 32, 52

September 12-18, 2011

Kodi Mpumulo wa Mulungu N’chiyani?

TSAMBA 24

NYIMBO ZOIMBA: 19, 27

September 19-25, 2011

Kodi Mwalowa mu Mpumulo wa Mulungu?

TSAMBA 28

NYIMBO ZOIMBA: 55, 24

Cholinga cha Nkhani Zophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 TSAMBA 10-19

Yehova amatichenjeza mwachikondi za zinthu zoipa zimene zingatisocheretse pa njira yopita ku moyo wosatha. Nkhani ziwirizi zikufotokoza zinthu 6 zimene zingatisocheretse ndiponso mmene tingazipewere.

NKHANI ZOPHUNZIRA 3, 4 TSAMBA 24-32

Baibulo limanena kuti Yehova atalenga anthu “anapuma” pa tsiku la 7. (Aheb. 4:4) Pa nkhani ziwirizi, yoyamba ikufotokoza cholinga cha tsiku la mpumulo wa Mulungu ndiponso chifukwa chake lili lofunika kwa ife. Nkhani yachiwiri ikufotokoza njira zina zimene tingasonyezere kuti talowa nawo mu mpumulo wa Yehova.

M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI

3 Nsanja ya Olonda Yatsopano ya M’Chingelezi Chosavuta

4 Anthu a Yehova Awina Milandu Imene Yatenga Nthawi Yaitali

20 Ndinkaopa Imfa Koma Tsopano Ndikuyembekezera ‘Moyo Wochuluka’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena