Zamkatimu
August 15, 2011
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
September 26, 2011–October 2, 2011
TSAMBA 8
October 3-9, 2011
TSAMBA 12
October 10-16, 2011
Yehova Ndi “Mulungu Amene Amapatsa Mtendere”
TSAMBA 23
October 17-23, 2011
Yesetsani Kukhala pa Mtendere ndi Ena
TSAMBA 27
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 TSAMBA 8-16
M’Malemba Achiheberi muli maulosi ambiri onena za Mesiya. Kuphunzira ena mwa maulosiwa kungatithandize kuzindikira Mesiya amene Mulungu analonjeza. Nkhani zimenezi zitithandiza mu utumiki. Ndipo mfundo za m’nkhanizi zitithandizanso kukhulupirira kwambiri maulosi a m’Mawu a Mulungu.
NKHANI ZOPHUNZIRA 3, 4 TSAMBA 23-31
Mgwirizano wa Mboni za Yehova ndi wapadera ndipo tiyenera kuuyamikira nthawi zonse. Nkhani yoyamba ikufotokoza zitsanzo za m’Baibulo zotilimbikitsa kukhala anthu okonda mtendere. Nkhani yachiwiri isonyeza zimene tingachite kuti tizikhala pa mtendere ndi anthu ena.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
3 Tiyenera Kugwiritsa Ntchito Intaneti Mwanzeru
6 Njira Zopangira Kulambira kwa Pabanja Kapena Kuphunzira Baibulo Patokha
17 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
18 Msonkhano Wapadera Komanso Wosaiwalika
22 Mafunso Ochokera kwa Owerenga