Zamkatimu
June 15, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino ndi wathu.
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA
JULY 30, 2012–AUGUST 5, 2012
TSAMBA 7 • NYIMBO: 114, 117
AUGUST 6-12, 2012
Yehova Waulula “Zimene Ziyenera Kuchitika Posachedwapa”
TSAMBA 14 • NYIMBO: 116, 54
AUGUST 13-19, 2012
Kodi Mumaika Kutumikira Yehova pa Malo Oyamba?
TSAMBA 20 • NYIMBO: 66, 103
AUGUST 20-26, 2012
‘Anatsogoleredwa ndi Mzimu Woyera’
TSAMBA 25 • NYIMBO: 37, 95
CHOLINGA CHA NKHANI ZOPHUNZIRA
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 TSAMBA 7-18
Kodi ndi maulosi ati a m’Baibulo amene angakuthandizeni kudziwa zimene zidzachitike padzikoli m’tsogolo? Nkhani ziwirizi zikufotokoza bwino ulosi wa chifaniziro chachikulu chotchulidwa m’buku la Danieli chaputala 2. Zikufotokozanso chilombo ndi chifaniziro chake chotchulidwa m’Chivumbulutso chaputala 13 ndi 17. Muona nokha kuti Baibulo limatithandizadi kudziwa zam’tsogolo.
NKHANI YOPHUNZIRA 3 TSAMBA 20-24
Mkhristu wobatizidwa aliyense amakhala atalonjeza kuti aziika patsogolo chifuniro cha Mulungu. Kuganizira zimene atumiki akale okhulupirika anasankha pa moyo wawo kukhoza kutithandiza kuona ngati tikugwiritsa ntchito bwino nthawi, mphamvu ndiponso chuma chathu.
NKHANI YOPHUNZIRA 4 TSAMBA 25-29
Olemba Baibulo ndiponso aneneri anatsogoleredwa ndi mzimu wa Mulungu. Nkhaniyi ikufotokoza mmene izi zinachitikira komanso ikupereka maumboni otsimikizira kuti Baibulo ndi lochokera kwa Mulungu. (2 Pet. 1:21) Ikufotokozanso zimene zingatithandize kuti tiziyamikirabe Baibulo.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
3 “Chinsinsi” Chimene Taphunzira Potumikira Mulungu
19 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
30 Muzifufuza “Nzeru Zoyendetsera Moyo” Wanu
32 Kukomera Mtima Munthu Wokwiya Kumathandiza
PATSAMBA LOYAMBA: Kuti afikire anthu ambiri, amalalikira m’malo osiyanasiyana. Mwachitsanzo, amalalikira mumsika wa m’madzi kudera lotchedwa Damnoen Saduak.
THAILAND
KULI ANTHU OKWANA
66,720,000
KULI OFALITSA OKWANA
3,423
APAINIYA OKHAZIKIKA
824