Zamkatimu
February 15, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
MAGAZINI YOPHUNZIRA
APRIL 1-7, 2013
Cholowa Chathu Chochokera kwa Mulungu
TSAMBA 3 • NYIMBO: 69, 28
APRIL 8-14, 2013
Kodi Timayamikira Cholowa Chathu Chochokera kwa Mulungu?
TSAMBA 8 • NYIMBO: 22, 75
APRIL 15-21, 2013
Khalanibe Otetezeka M’chigwa cha Yehova
TSAMBA 17 • NYIMBO: 133, 16
APRIL 22-28, 2013
Musalole Chilichonse Kukulepheretsani Kupeza Ulemerero
TSAMBA 25 • NYIMBO: 15, 61
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Cholowa Chathu Chochokera kwa Mulungu
▪ Kodi Timayamikira Cholowa Chathu Chochokera kwa Mulungu?
M’nkhani ziwirizi, tikambirana zinthu zofunika kwambiri zokhudza cholowa chathu chochokera kwa Yehova. Zikusonyeza mmene Mulungu watetezera Mawu ake, mmene wadalitsira anthu amene amagwiritsa ntchito dzina lake komanso mmene watetezera choonadi kuti tisasocheretsedwe ndi mabodza amene zipembedzo zimaphunzitsa.
▪ Khalanibe Otetezeka M’chigwa cha Yehova
Nkhaniyi ikufotokoza za “chigwa” chachitetezo chotchulidwa pa Zekariya 14:4. Ikusonyezanso chifukwa chake tiyenera kukhalabe m’chigwachi. Ikufotokozanso tanthauzo la “madzi amoyo” otchulidwa pa Zekariya 14:8 komanso mmene madziwa angatithandizire.
▪ Musalole Chilichonse Kukulepheretsani Kupeza Ulemerero
Nkhaniyi ikusonyeza mmene tingapezere ulemerero wochokera kwa Yehova. Ikufotokozanso zinthu zimene zingatilepheretse kuupeza komanso mmene tingathandizire ena kupeza ulemererowu.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
13 Paulo Analalikira Msilikali Woteteza Mfumu
22 Samalani ndi Zolinga za Mtima Wanu
30 Anali Wochokera M’banja la Kayafa
31 Kale Lathu
TSAMBA LOYAMBA: Wofalitsa wa kumpoto chakum’mwera kwa Namibia akulalikira kwa mayi wachihimba. Anthu achihimba amakonda kuyendayenda ndi ziweto. Azimayi amadzola ndiponso kupaka tsitsi lawo mafuta enaake amene amawasakaniza ndi dothi lochokera ku miyala inayake
NAMIBIA
KULI ANTHU
2,373,000
KULI OFALITSA
2,040
MAPHUNZIRO A BAIBULO
4,192