Zamkatimu
March 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
MAGAZINI YOPHUNZIRA
MAY 5-11, 2014
Kodi Tingatani Kuti Tikhalebe ndi Mtima Wodzipereka?
TSAMBA 7 • NYIMBO: 61, 25
MAY 12-18, 2014
Kodi Tingatani Kuti Tikhalebe Osangalala?
TSAMBA 12 • NYIMBO: 74, 119
MAY 19-25, 2014
TSAMBA 20 • NYIMBO: 90, 135
MAY 26, 2014–JUNE 1, 2014
Kodi Achikulire Tingawasamalire Bwanji?
TSAMBA 25 • NYIMBO: 134, 29
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Kodi Tingatani Kuti Tikhalebe ndi Mtima Wodzipereka?
Tili ndi mdani wochenjera amene safuna kuti tizitumikira Mulungu modzipereka. Nkhaniyi itithandiza kudziwa mdani ameneyu komanso mmene tingagwiritsire ntchito Baibulo polimbana naye.
▪ Kodi Tingatani Kuti Tikhalebe Osangalala?
Kukhalabe wosangalala kungatithandize kupirira pamene tikulambira Yehova. N’chifukwa chiyani anthu ena amadziona kuti ndi achabechabe? Nkhaniyi itisonyeza mmene Baibulo lingatithandizire kuti tikhalebe osangalala.
▪ Muzilemekeza Anthu Achikulire
▪ Kodi Achikulire Tingawasamalire Bwanji?
Nkhanizi zikufotokoza udindo umene Mkhristu aliyense komanso mpingo uli nawo posamalira Akhristu anzathu kapena achibale okalamba. Tionanso zimene tingachite kuti tikwanitse udindo umenewu.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
3 Kodi Tingathandize Bwanji Achibale Omwe Si Mboni?
PATSAMBA LOYAMBA: Abale ndi alongo ena ku Australia amayenda mtunda wautali kuti akalalikire kwa alimi a ng’ombe
AUSTRALIA
KULI ANTHU OKWANA
23,192,500
KULI OFALITSA OKWANA
66,967