Zamkatimu
November 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
DECEMBER 29, 2014–JANUARY 4, 2015
Kodi Kuuka kwa Yesu Kumatithandiza Bwanji?
TSAMBA 3 • NYIMBO: 5, 60
JANUARY 5-11, 2015
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Oyera?
TSAMBA 8 • NYIMBO: 119, 17
JANUARY 12-18, 2015
Tikhale Oyera M’makhalidwe Athu Onse
TSAMBA 13 • NYIMBO: 65, 106
JANUARY 19-25, 2015
“Anthu Amene Mulungu Wawo Ndi Yehova”
TSAMBA 18 • NYIMBO: 46, 63
JANUARY 26, 2015–FEBRUARY 1, 2015
“Tsopano Ndinu Mtundu wa Anthu a Mulungu”
TSAMBA 23 • NYIMBO: 112, 101
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Kodi Kuuka kwa Yesu Kumatithandiza Bwanji?
Nkhaniyi ikufotokoza umboni wotitsimikizira kuti Yesu anaukitsidwa ndipo adakali moyo. Kudziwa zimenezi kungatilimbikitse ndiponso kutithandiza pa ntchito yathu yolalikira.
▪ N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Oyera?
▪ Tikhale Oyera M’makhalidwe Athu Onse
Nkhanizi zikuchokera m’buku la Levitiko ndipo zikuyankha mafunso awa: N’chifukwa chiyani Yehova amafuna kuti tizikhala oyera? Kodi tingakhale bwanji oyera? Kodi tingasonyeze bwanji kuti ndife oyera m’makhalidwe athu onse?
▪ “Anthu Amene Mulungu Wawo Ndi Yehova”
▪ “Tsopano Ndinu Mtundu wa Anthu a Mulungu”
Anthu ena amene timaphunzira nawo Baibulo sakhulupirira kuti Yehova ali ndi gulu limodzi padzikoli. Iwo amaganiza kuti munthu wa m’chipembedzo chilichonse akhoza kusangalatsa Mulungu ngati akumulambira mochokera pansi pa mtima. Nkhanizi zikusonyeza kuti munthu ayenera kuzindikira anthu a Mulungu ndiponso kugwirizana nawo pomutumikira.
PATSAMBA LOYAMBA: Akulalikira mumzinda waukulu wa Santiago de Cuba. Mzindawu uli pachilumba cha Cuba chomwe chimadziwika ndi nyimbo komanso magule
CUBA
KULI ANTHU
11,163,934
KULI OFALITSA
96,206
KULI APAINIYA OKHAZIKIKA
9,040