Zamkatimu
December 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
FEBRUARY 2-8, 2015
‘Mverani Ndipo Mumvetse Tanthauzo Lake’
TSAMBA 6 • NYIMBO: 92, 120
FEBRUARY 9-15, 2015
Kodi Timamvetsa Tanthauzo Lake?
TSAMBA 11 • NYIMBO: 97, 96
FEBRUARY 16-22, 2015
Tizigwirizana Kwambiri Pamene Mapeto Akuyandikira
TSAMBA 22 • NYIMBO: 107, 29
FEBRUARY 23, 2015–MARCH 1, 2015
Kodi Mumayamikira Zimene Muli Nazo?
TSAMBA 27 • NYIMBO: 89, 135
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ ‘Mverani Ndipo Mumvetse Tanthauzo Lake’
▪ Kodi Timamvetsa Tanthauzo Lake?
Kodi tingatani kuti timvetse bwino mafanizo a Yesu? Nkhani ziwirizi zitithandiza kumvetsetsa mafanizo 7 a Yesu. Zitithandizanso kudziwa mmene tingagwiritsire ntchito zimene taphunzira pa mafanizowa pokambirana ndi anthu mu utumiki.
▪ Tizigwirizana Kwambiri Pamene Mapeto Akuyandikira
▪ Kodi Mumayamikira Zimene Muli Nazo?
M’dzikoli achinyamata ambiri ndi odzikonda. Koma achinyamata achikhristu ayenera kugwirizana kwambiri ndi gulu la Yehova. Nkhanizi zikufotokoza zitsanzo zabwino ndiponso zoipa. Zikufotokozanso mfundo zimene zingathandize achinyamata komanso achikulire kuti azisankha bwino zochita.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
4 Yehova Amadalitsa Anthu Opereka ndi Mtima Wonse
17 Kodi Ndi Bwino Kusintha Maganizo Anu?
PATSAMBA LOYAMBA: Anthu ena amene amapita ku Tamarindo m’mphepete mwa nyanja ya Pacific m’dziko la Costa Rica amasangalala kuphunzira kuti m’tsogolo dziko lonse lidzakhala paradaiso
COSTA RICA
KULI OFALITSA
29,185
KULI APAINIYA
2,858
Dzina la Mulungu lakuti Yehova,
Jéoba
mu chilankhulo cha Chibiribiri
Jehová
mu chilankhulo cha Chikabeka
Kuli mipingo iwiri ndiponso timagulu tiwiri mu chilankhulo cha Chibiribiri ndipo kuli mipingo itatu ndiponso timagulu 4 mu Chikabeka