Zamkatimu
September 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
OCTOBER 26, 2015–NOVEMBER 1, 2015
Kodi Mukuyesetsa Kukhala Ngati Khristu?
TSAMBA 3
NOVEMBER 2-8, 2015
Kodi Chikumbumtima Chanu Chimakuthandizani Kusankha Zochita Mwanzeru?
TSAMBA 8
NOVEMBER 9-15, 2015
Khalani ndi Chikhulupiriro Cholimba
TSAMBA 13
NOVEMBER 16-22, 2015
Kodi Yehova Amasonyeza Bwanji Kuti Amatikonda?
TSAMBA 18
NOVEMBER 23-29, 2015
Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Yehova?
TSAMBA 23
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Kodi Mukuyesetsa Kukhala Ngati Khristu?
▪ Kodi Chikumbumtima Chanu Chimakuthandizani Kusankha Zochita Mwanzeru?
M’nkhanizi tiona zimene tingachite polimbitsa ubwenzi wathu ndi Mulungu n’cholinga choti tikhale Akhristu olimba. Tionanso zimene tingachite pophunzitsa chikumbumtima chathu kuti chizititsogolera bwino posankha zochita.
▪ Khalani ndi Chikhulupiriro Cholimba
Tsiku lina Petulo anayesa kuyenda panyanja ya Galileya koma chikhulupiriro chake chitachepa anayamba kumira. M’nkhaniyi tiona zinthu zimene zingatithandize kudziwa ngati chikhulupiriro chathu chayamba kuchepa komanso zimene tingachite kuti tichilimbitse.
▪ Kodi Yehova Amasonyeza Bwanji Kuti Amatikonda?
▪ Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Yehova?
Tikadziwa zoti Yehova amatikonda ndipo nafenso n’kumamukonda, timasangalala kwambiri. Nkhani ziwirizi zikusonyeza umboni wakuti Yehova amatikonda komanso zimene tingachite posonyeza kuti timamukonda.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IYI
PATSAMBA LOYAMBA: Abale ndi alongo a ku Italy amene ali mumpingo wachitchainizi akulalikira kwa anthu obwera mumzinda wa Rome. Abale ndi alongowa amaika mashelefu a matayala pafupi ndi nyumba zakale zotchuka ndipo anthu ambiri amabwera kudzatenga mabuku
ITALY
KULI ANTHU
60,782,668
KULI OFALITSA
251,650
KULI APAINIYA
33,073
Abale ndi alongo oposa 24,000 amalalikira m’zilankhulo zakunja zokwana 37