Magazini Yophunzira
AUGUST 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: SEPTEMBER 26 MPAKA OCTOBER 23, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
HUNGARY
Zimakhala zosangalatsa abale ndi alongo akamalalikira m’mawa m’mbali mwa mtsinje wa Danube. Apa alongo akulalikira kwa munthu wachidwi amene amupeza m’dera lotchedwa Vigadó Square ku Budapest.
KULI OFALITSA
22,582
KULI APAINIYA
1,980
MAPHUNZIRO A BAIBULO
12,163
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.pr2711.com/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.