Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
3 Mbiri ya Moyo Wanga—Ndimasangalala Chifukwa Chothandiza Ena
MLUNGU WA SEPTEMBER 26, 2016–OCTOBER 2, 2016
8 Kodi Ukwati Unayamba Bwanji Nanga Cholinga Chake N’chiyani?
MLUNGU WA OCTOBER 3-9, 2016
13 Kodi Mungatani Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino?
Nkhani yoyamba ikufotokoza mmene ukwati unayambira ndiponso zimene Chilamulo cha Mose chinkanena pa nkhaniyi. Ikufotokozanso malangizo okhudza ukwati amene Yesu anapereka kwa Akhristu. Nkhani yachiwiri ikufotokoza udindo wa mwamuna komanso wa mkazi m’banja.
18 Muzifufuza Chuma Chamtengo Wapatali Kuposa Golide
MLUNGU WA OCTOBER 10-16, 2016
20 Kodi Tingatani Kuti Tizichita Zambiri M’gulu la Yehova?
MLUNGU WA OCTOBER 17-23, 2016
25 Kodi Kuphunzitsa Ena N’kofunika Bwanji?
Tonsefe tikusangalala kuona kuti ntchito yolalikira ikuyenda bwino. Koma kodi tikudziwa kuti zimenezi zikupangitsa kuti m’gulu la Yehova mukhale ntchito yambiri? Kodi tingatani kuti tizichita zambiri m’gulu la Yehova? Nanga tingathandize bwanji amene timaphunzira nawo kuti nawonso azichita zambiri? N’chifukwa chiyani tiyenera kuphunzitsa ena? M’nkhanizi tikambirana mayankho a mafunso amenewa.
30 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
31 Kale Lathu