Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
3 Mbiri ya Moyo Wanga-Ndimayesetsa Kutengera Anthu a Zitsanzo Zabwino
MLUNGU WA NOVEMBER 28, 2016–DECEMBER 4, 2016
8 “Musaiwale Kuchereza Alendo”
MLUNGU WA DECEMBER 5-11, 2016
13 Mungatani Kuti Mukhalebe Olimba Mwauzimu mu Mpingo wa Chilankhulo China?
Masiku ano m’mipingo yambiri mukumapezeka anthu a chilankhulo china kapena ochokera m’mayiko ena. Nkhani yoyamba ikufotokoza mmene tingathandizire anthu oterewa amene timasonkhana nawo mu mpingo wathu. Nkhani yachiwiri ikufotokoza zimene Akhristu ochokera m’mayiko ena angachite kuti akhalebe olimba mwauzimu.
18 Kodi ‘Mumasunga Nzeru Zopindulitsa’?
MLUNGU WA DECEMBER 12-18, 2016
21 Muzikhulupirira Kwambiri Zinthu Zimene Mukuyembekezera
MLUNGU WA DECEMBER 19-25, 2016
26 Muzisonyeza Kuti Mumakhulupirira Malonjezo a Yehova
Nkhanizi zikufotokoza tanthauzo la chikhulupiriro limene lafotokozedwa pa Aheberi 11:1. Nkhani yoyamba ikufotokoza zimene tingachite kuti tikhale ndi chikhulupiriro cholimba. Nkhani yachiwiri ikusonyeza kuti kukhala ndi chikhulupiriro sikumangotanthauza kumvetsa malonjezo a Mulungu.