Magazini Yophunzira
OCTOBER 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: NOVEMBER 28 MPAKA DECEMBER 25, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
LUXEMBOURG
Abale akulalikira makaniko pagalaja. Akugwiritsa ntchito kapepala kakuti, Kodi Baibulo Mumalikhulupira? pofuna kumuthandiza kuti azikonda Mawu a Mulungu
KULI ANTHU
562,958
KULI OFALITSA
2,058
OPEZEKA PACHIKUMBUTSO (2015)
3,895
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.