Magazini Yophunzira
November 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA DECEMBER 26, 2016 MPAKA JANUARY 29, 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
ANGOLA
Apainiya apadera akuchititsa phunziro la Baibulo m’chinenero chamanja mumzinda wa Benguela pogwiritsa ntchito kabuku kakuti, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha. Ofalitsa 10 amumzindawu, omwe ali ndi vuto losamva, anasangalala kwambiri pamene anthu okwana 62 anafika pa Chikumbutso mu 2015.
KULI OFALITSA
115,948
MAPHUNZIRO A BAIBULO
502,848
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2015)
529,827
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.