Magazini Yophunzira
APRIL 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JUNE 4–JULY 8, 2018
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
KYRGYZSTAN
Banja limene likuchita upainiya wapadera likulalikira m’dera lakumidzi pafupi ndi mzinda wa Balykchy
KULI OFALITSA
5,235
MAPHUNZIRO A BAIBULO
4,653
OPEZEKA PACHIKUMBUTSO (2017)
10,067
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.pr2711.com/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.