Nkhani Zimene Zili M’Magaziniyi
3 Mbiri ya Moyo Wanga—Ndinali Wosauka Koma Panopa Ndine Wolemera
9 Mtendere, Kodi Mungaupeze Bwanji?
MLUNGU WA JULY 9-15, 2018
12 Yehova Amakonda Anthu Amene ‘Amabereka Zipatso’ Mopirira
MLUNGU WA JULY 16-22, 2018
17 N’chifukwa Chiyani Tiyenera ‘Kupitiriza Kubala Zipatso Zambiri’?
Nkhani yoyamba ikufotokoza fanizo la Yesu lonena za mtengo wa mpesa komanso la wofesa mbewu ndipo ikusonyeza zimene tikuphunzira zokhudza ntchito yolalikira. Nkhani yachiwiri ikufotokoza zifukwa zingapo za m’Malemba zotichititsa kugwira ntchito yolalikira mopirira.
MLUNGU WA JULY 23-29, 2018
22 Kodi Mumamudziwa Bwino Mdani Wanu?
MLUNGU WA JULY 30, 2018–AUGUST 5, 2018
27 Achinyamata, Musasunthike Polimbana ndi Mdyerekezi
Satana ndi mdani wathu. Koma kodi ali ndi mphamvu zotani? Nanga kodi alibe mphamvu yochita zinthu ziti? Ndipo kodi n’chiyani chingatithandize tonsefe, kuphatikizapo achinyamata, kuti tilimbane naye? Nkhani ziwirizi ziyankha mafunso amenewa ndipo zitilimbikitsa kuti tikhale osasunthika polimbana ndi Mdyerekezi.