Magazini Yophunzira
MAY 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JULY 9–AUGUST 5, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
SIERRA LEONE
Pa nyengo yamvula, apainiya awiri akugawira kapepala kwa munthu amene akudutsa mumzinda wa Freetown womwe ndi likulu la dzikoli
KULI OFALITSA
2,171
MAPHUNZIRO A BAIBULO
5,291
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2017)
8,831
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.