Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw.Org
TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO
Yonatani—“Palibe Chimene Chingalepheretse Yehova”
Yonatani ndi mnzake mmodzi yekha anamenyana ndi gulu la asilikali la Afilisiti ndipo zotsatira zake zinali zosaiwalika.
(Pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUKHULUPIRIRA MULUNGU.)
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Ndinagwirizana ndi Bambo Anga Patatha Zaka Zambiri
Ali ndi zaka 14, Renée anachoka pakhomo chifukwa cha nkhanza za bambo ake. Kodi n’chiyani chinathandiza kuti iye ndi bambo ake agwirizanenso patapita zaka zambiri?
(Pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MTENDERE KOMANSO MOYO WOSANGALALA.)