Lipoti Lautumiki la March
Av. Av. Av. Av.
Chiŵerengero cha: Maola Mag. M.O. Maph.
Apai. Apad. 4 151.8 17.8 101.0 9.3
Apainiya 2,722 88.4 2.6 33.5 3.0
Apai. Otha. 3,557 57.7 2.1 20.4 1.9
Ofalitsa 34,246 11.4 0.2 4.3 0.5
PAMODZI 40,529* Obatizidwa: 0
*Chimenechi ndicho chiŵerengero chapamwamba chatsopano cha ofalitsa m’Malaŵi, ndipo ndi kuwonjezeka kwa 13 peresenti kuposa avareji ya chaka chatha chautumiki. Tinalinso ndi ziŵerengero zapamwamba zatsopano za apainiya okhazikika ndi othandiza, maola, maulendo obwereza ndi maphunziro a Baibulo. Tikuthokozani kwambiri abale ndi alongo!