Phunziro la Buku la Mpingo
Ndandanda ya maphunziro a mpingo m’buku la Ogwirizana m’Kulambiridwa kwa Mulungu Yekha Wowona.
February 1: Mas. 80, ndime 7 mpaka 82, ndime 12
February 8: Mas. 83, ndime 13 mpaka 90, ndime 8
February 15: Mas. 91 mpaka 94
February 22: Mas. 95 mpaka 98, ndime 8
March 1: Mas. 98, ndime 9 mpaka 102
March 8: Mas. 103 mpaka 105, ndime 5
March 15: Mas. 106, ndime 6 mpaka 110
* Ndime zophunziridwa zagaŵidwa mogwirizana ndi kuchuluka kwa malemba amene agwiritsidwa ntchito. Ayenera kuŵerengedwa ndi kuwasonyeza mmene angagwiritsidwire ntchito ngati nthaŵi ilola.