Ndandanda ya Mlungu wa May 18
MLUNGU WOYAMBIRA MAY 18
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 19 ndime 9-17
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Eksodo 30–33
Na. 1: Eksodo 31:1-18
Na. 2: Chifukwa Chake Akhristu Oyambirira Anapatsidwa Mphatso za Kuchiritsa (rs-CN tsa. 169 ndime 1-4)
Na. 3: Kodi Mumakumbukira Kunena Kuti Zikomo? (lr-CN mutu 18)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph.5: Zilengezo.
Mph.10: Dzina la Mulungu Ndilo Linga Lolimba. Nkhani yochokera pa mfundo za pakamutu kachiwiri ka patsamba 274 m’buku la Sukulu ya Utumiki.
Mph.10: Zinthu Zitatu Zothandiza Kupeza Mawu Oyamba Abwino. Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera m’buku la Kukambitsirana patsamba 9, ndime 1. Pomaliza kukambirana mfundozo, chitani chitsanzo chosonyeza mmene tingayambire kulankhula ndi anthu pogawira buku m’mwezi wa June.
Mph.10: “Kodi Tingakonzekere Bwanji Msonkhano wa Utumiki?” Nkhani yokambirana mwa mafunso ndi mayankho.