Ndandanda ya Mlungu wa August 3
MLUNGU WOYAMBIRA AUGUST 3
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 23 ndime 10-18
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Numeri 4-6
Na. 1: Numeri 4:1-16
Na. 2: Kudziwa Amene Tiyenera Kumumvera (lr-CN mutu 28)
Na. 3: Kodi Munthu Afunika Kupita Kumwamba Kuti Akhale ndi Tsogolo Labwinodi? (rs-CN tsa. 204 ndime 5 mpaka tsa. 205 ndime 1)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph.5: Zilengezo.
Mph.10: “Kodi Mungawonjezere Zimene Mumachita mu Utumiki?” Kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.
Mph.10: Zosowa za pampingo.
Mph.10: Dalirani Yehova Kuti Mukhale ndi Luso la Kuphunzitsa. Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 56 ndime 1 mpaka tsamba 57 ndime 2.