Ndandanda ya Mlungu wa September 7
MLUNGU WOYAMBIRA SEPTEMBER 7
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 25, ndime 12-21, ndi bokosi, tsa. 259
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Numeri 22-25
Na. 1: Numeri 22:20-35
Na. 2: Mmene Yesu Anatetezedwera (lr-CN mutu 32)
Na. 3: Kodi Lemba la 1 Petulo 4:6 Limatanthauza Chiyani? (rs-CN tsa. 205, ndime 3)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph.5: Zilengezo.
Mph.10: Kuyankha Mafunso Okhudza Masiku Otsiriza. Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera m’buku la Kukambitsirana, tsamba 268, ndime 6, mpaka tsamba 270, ndime 2. Chitani chitsanzo chosonyeza mmene mungagwiritsire ntchito mfundo imodzi ya m’nkhaniyi.
Mph.10: Zosowa za pampingo.
Mph.10: Njira Zothandiza Zofufuzira Oyenerera. Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera m’buku la Gulu, tsamba 95, ndime 3, mpaka tsamba 96, ndime 3. Pemphani ofalitsa kuti afotokoze kapena kuchita chitsanzo chimodzi kapena ziwiri za zinthu zochititsa chidwi zimene zinachitika pamene ankalalikira m’gawo lawo pogwiritsa ntchito njira zina zochitira umboni.