Ndandanda ya Mlungu wa November 30
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 30
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 30, ndime 8-14
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Deuteronomo 32-34
Na. 1: Deuteronomo 32:1-21
Na. 2: Kodi “Tsiku Lalikulu la Yehova” N’chiyani? (Zef. 1:14)
Na. 3: Kodi Abale Athu ndi Alongo Athu Ndani? (lr-CN mutu 43)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Mabuku Ogawira mu December. Chitani chitsanzo chosonyeza mmene banja lingakonzekerere zokanena mu utumiki wakumunda. Bambo achite zimene wakonzekera kukachita mu utumiki, kenako winanso m’banjamo achite zimene wakonza kukachita mu utumiki wakumunda.
Mph. 10: “Ndife Mboni za Yehova Nthawi Zonse.” Kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.
Mph. 10: “Mmene Tingagwiritsire Ntchito Buku la ‘Chikondi cha Mulungu’ Pochititsa Maphunziro a Baibulo.” Mawu anu oyamba asafike mphindi imodzi, ndiyeno kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.