Ndandanda ya Mlungu wa January 18
MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 18
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Oweruza 1-4
Na. 1: Oweruza 2:11-23
Na. 2: Kodi ndi Anthu Otani Amene Amapita ku Helo Wotchulidwa M’Baibulo? (rs tsa. 145 ndime 2 mpaka 4)
Na. 3: Mulungu Sanalenge Mdyerekezi
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: Konzekerani Kugawira Magazini ya Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! Fotokozani mwachidule mfundo za m’magaziniwa ndipo funsani omvera kuti atchule nkhani zimene akuona kuti zingachititse chidwi anthu m’gawo lanu. Chitani chitsanzo chosonyeza wofalitsa wamng’ono akukonzekera kugawira magazini.
Mph. 15: Bokosi la Mafunso. Nkhani yokambirana ndi omvera. Werengani malemba osagwidwa mawu ndipo kambiranani.