Ndandanda ya Mlungu wa November 15
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 15
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 1 Mbiri 26-29
Na. 1: 1 Mbiri 29:10-19
Na. 2: Kodi N’chifukwa Chiyani Mfundo Zina za Ziphunzitso za Mboni za Yehova Zakhala Zikusintha? (rs tsa. 277 ndime 1)
Na. 3: Kodi Ayuda Onse Adzatembenuka N’kukhala Akhristu?
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: “‘Uzilemekeza Yehova ndi Zinthu Zako Zamtengo Wapatali’—Gawo 2.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho.
Mph. 15: “Bwera Ukhale Wotsatira Wanga.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho.