Ndandanda ya Mlungu wa February 7
MLUNGU WOYAMBIRA FEBRUARY 7
Nyimbo Na. 25 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 2 ndime 9-14 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Nehemiya 5-8 (Mph. 10)
Na. 1: Nehemiya 6:1-13 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Tingaphunzire Chiyani kwa Lidiya, Gayo ndi Filimoni pa Nkhani ya Kuchereza Alendo? (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Mawu Odabwa a Tomasi a pa Yohane 20:28 Amatsimikizira Kuti Yesu Ndi Mulungu?—rs tsa. 427 ndime 2 mpaka 4 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Kodi Mukugwiritsa Ntchito Mphatso Yanu mu Utumiki? Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki tsamba 75, ndime 4, mpaka tsamba 76, ndime 2.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Muzinena Zoona Polalikira Ndi Pophunzitsa. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 223, ndime 1 mpaka 5.
Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero