Ndandanda ya Mlungu wa April 4
MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 4
Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 5 ndime 1-8 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yobu 16–20 (Mph. 10)
Na. 1: Yobu 18:1-21 (osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Yesu Atapita Kumwamba Anakakhala ndi Thupi Limene Anali Nalo Padziko Lapansi?—rs tsa. 431 ndime 3-6 (Mph. 5)
Na. 3: N’chifukwa Chiyani Olamulira Ozindikira Amayamikira Mboni za Yehova?—Aroma 13:3 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: “Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira.” Nkhani yokambirana. Konzeranitu kuti ena adzafotokoze zokumana nazo zolembedwa m’mabuku athu zimene zawalimbikitsa.
Mph. 15: “Uzilemekeza Yehova ndi Zinthu Zako Zamtengo Wapatali—Gawo 3.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho.
Nyimbo Na. 45 ndi Pemphero