Ndandanda ya Mlungu wa May 16
MLUNGU WOYAMBIRA MAY 16
Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 7 ndime 1-8 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Masalimo 11-18 (Mph. 10)
Na. 1: Salimo 17:1-15 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Mmene Tingasonyezere Kuti Timalambira Yehova Yekha—Aroma 6:16, 17 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Ayuda Enieni Ndiwo Anthu Osankhidwa a Mulungu Masiku Ano?—rs tsa. 42 ndime 2 mpaka tsa. 43 ndime 4 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Gwiritsani Ntchito Mafunso Kuti Muziphunzitsa Mogwira Mtima: Gawo 1. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 236 mpaka 237 ndime 2. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza mmene mungagwiritsire ntchito mfundo imodzi kapena ziwiri za m’nkhaniyo.
Mph. 10: Njira Zolalikirira Uthenga Wabwino: Kupanga Maulendo Obwereza. Nkhani yochokera m’buku la Gulu, tsamba 97 ndime 1 mpaka 3. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza mkulu akuchita ulendo wobwereza kwa munthu amene walandira buku kapena magazini amene mukugawira mwezi umenewo.
Mph. 10: “Muzionetsetsa Kuti Mukulalikira Nawo Lamlungu.” Mafunso ndi mayankho.
Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero