Ndandanda ya Mlungu wa August 22
MLUNGU WOYAMBIRA AUGUST 22
Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 11, ndime 15-21 ndi bokosi patsamba 117 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Masalimo 106–109 (Mph. 10)
Na. 1: Salimo 109:1-20 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Ufumu wa Mulungu Udzabweretsa Chilungamo Padziko Lonse—rs tsa. 379 ndime 3-5 (Mph. 5)
Na. 3: Tsatirani Yehova ndi Yesu Pokhala Aulemu (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 10: Zilengezo. ‘Chifuniro cha Mulungu Chichitike.’ Mafunso ndi mayankho. Lengezani tsiku la msonkhano wapadera ngati likudziwika.
Mph. 25: “Kodi ‘Mungawolokere ku Makedoniya’?” Onani tsamba 4. Mafunso ndi mayankho. Ngati alipo, funsani wofalitsa amene anasamulira kudera lina pofuna kupititsa patsogolo ntchito yolalikira uthenga wabwino.
Nyimbo Na. 1 ndi Pemphero