Ndandanda ya Mlungu wa December 19
MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 19
Nyimbo Na. 25 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 17 ndime 10-15 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yesaya 11-16 (Mph. 10)
Na. 1: Yesaya 13:1-16 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: N’chifukwa Chiyani ‘Timayenda mwa Chikhulupiriro, Osati mwa Zooneka ndi Maso’?—2 Akor. 5:7 (Mph. 5)
Na. 3: Ngati Wina Anena Kuti: “Sikuti Zinthu Zafika Poipa Kwambiri Masiku Ano. Nkhondo, Njala, Zivomezi ndi Umbanda Zakhala Zikuchitika Kuyambira Kalekale”—rs tsa. 268 ndime 6 mpaka tsa. 269 ndime 2 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 10: Zilengezo. Tchulani mabuku ogawira m’mwezi wa January ndipo chitani chitsanzo chimodzi.
Mph. 15: Mzimu Woyera Umatipatsa Mphamvu Kuti Tizilalikira Molimba Mtima. Nkhani yokambirana yochokera mu Nsanja ya Olonda ya July 15, 2009, tsamba 22 ndi 23, ndime 12 mpaka 18. Pemphani omvera kuti afotokoze zimene aphunzirapo.
Mph. 10: Bokosi la Mafunso. Nkhani yokambirana yokambidwa ndi woyang’anira utumiki.
Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero