Ndandanda ya Mlungu wa December 26
MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 26
Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 17 ndime 16-20 ndi bokosi patsamba 181 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yesaya 17-23 (Mph. 10)
Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu (Mph. 20)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo. Kambiranani nkhani yakuti, “Zimene Tingachite Kuti Tizisangalala ndi Nyimbo za Ufumu.”
Mph. 15: Mmene Mungagwiritsire Ntchito Buku la Kukambitsirana za m’Malemba. Nkhani yochokera m’buku la Kukambitsirana, tsamba 7 ndi 8. Fotokozani mmene mungagwiritsire ntchito mbali zosiyanasiyana za bukuli. Chitani chitsanzo chimodzi kapena ziwiri.
Mph. 15: Kodi Taphunzirapo Chiyani? Nkhani yokambirana. Werengani Machitidwe 10:1-35. Kambiranani mmene nkhani imeneyi ingatithandizire mu utumiki.
Nyimbo Na. 18 ndi Pemphero