Ndandanda ya Mlungu wa April 16
MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 16
Nyimbo Na. 68 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 4 ndime 13-20 ndi bokosi patsamba 34 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yeremiya 25-28 (Mph. 10)
Na. 1: Yeremiya 27:1-11 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Nkhani ya M’Baibulo Yonena za Mariya Imatiphunzitsa Chiyani?—rs tsa. 254 ndime 5 mpaka tsa. 255 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani Yolemekeza Okalamba? (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Kulitsani Luso la Kuphunzitsa—Gawo 3. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 59 mpaka 61.
Mph. 20: “Kusunga Mtendere ndi Chiyero cha Mpingo.” Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Gulu Lochita Chifuniro cha Yehova, tsamba 144 mpaka pa kamutu ka patsamba 150.
Nyimbo Na. 116 ndi Pemphero