Ndandanda ya Mlungu wa May 14
MLUNGU WOYAMBIRA MAY 14
Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 6 ndime 1-8 ndi bokosi patsamba 44 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yeremiya 39-43 (Mph. 10)
Na. 1: Yeremiya 40:1-10 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Anthu Angathe Kulowa mu Mpumulo wa Mulungu?—Aheb. 4:10, 11 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Mariya Anali Amayi a Mulungu?—rs tsa. 256 ndime 3 mpaka tsa. 257 ndime 2 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: Mwakutero, Onse Adzadziwa Kuti Ndinu Ophunzira Anga. (Yoh. 13:35) Nkhani yokambirana yochokera mu Nsanja ya Olonda ya March 1, 2012, patsamba 6. Pemphani omvera kuti anene mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’nkhaniyo pa zochitika zosiyanasiyana.
Mph. 15: “Muzisamala Mukakhala mu Utumiki.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho ndipo ikambidwe ndi woyang’anira utumiki. Fotokozani zimene mpingo ungachite m’gawo lanu potsatira malangizowa.
Nyimbo Na. 74 ndi Pemphero