Ndandanda ya Mlungu wa July 23
MLUNGU WOYAMBIRA JULY 23
Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero
❑ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 9 ndime 8-18 (Mph. 25)
❑ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Ezekieli 18–20 (Mph. 10)
Na. 1: Ezekieli 19:1-14 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Mmene Akhristu Amaonera Olamulira a Boma—rs tsa. 368 ndime 2 mpaka tsa. 369 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Lemba la Mateyu 21:43 Limatanthauza Chiyani? (Mph. 5)
❑ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: Muzigwiritsa Ntchito Mwaluso Zinthu Zooneka Pophunzitsa. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 247 mpaka 249 ndime 2. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza mmene tingagwiritsire ntchito mfundo imodzi kapena ziwiri zopezeka m’nkhaniyi.
Mph. 15: Yehova Amamva Mapemphero. (Sal. 66:19) Mafunso ndi mayankho. Kambiranani kuchokera m’buku la Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, mutu 17 ndime 16 mpaka 20. Gwiritsani ntchito mafunso amene ali pandimezo. Pemphani omvera kuti afotokoze mfundo zimene aphunzirapo.
Nyimbo Na. 56 ndi Pemphero