Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 9/13 tsamba 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa October 7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa October 7
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 7
Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
km 9/13 tsamba 4

Ndandanda ya Mlungu wa October 7

MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 7

Nyimbo Na. 62 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 2 ndime 1-6 , Tchati, patsamba 19 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Aefeso 1-6 (Mph. 10)

Na. 1: Aefeso 4:1-16 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Kodi Kufunafuna Choyamba Chilungamo cha Mulungu Kumatanthauza Chiyani?—Mat. 6:33 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi N’zoona Kuti Zipembedzo Zonse N’zabwino?—rs tsa. 84 ndime 3-tsa. 85 ndime 1 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 59

Mph. 10: Zimene Munganene Pogawira Magazini mu October. Nkhani yokambirana. Kwa masekondi 30 mpaka 60, fotokozani chifukwa chimene anthu a m’gawo lanu angakondere magaziniwo. Kenako, pogwiritsa ntchito nkhani zoyambirira za mu Nsanja ya Olonda, pemphani omvera kuti anene funso lochititsa chidwi lomwe angafunse ndiponso lemba limene angawerenge pogawira magaziniyo. Chitaninso chimodzimodzi ndi nkhani zoyambirira za m’magazini ya Galamukani! Ngati nthawi ilipo mungachitenso zimenezi ndi nkhani ina imodzi m’magazini ya Nsanja ya Olonda kapena Galamukani! Chitani chitsanzo chosonyeza mmene mungagawirire magazini iliyonse.

Mph. 10: Zosowa za pampingo.

Mph. 10: Akugwira Ntchito Mwakhama. (1 Ates. 5:12, 13) Funsani akulu awiri mafunso awa: Kodi amagwira ntchito yotani mu mpingo ndipo amachita mautumiki ena otani? Kodi amakwanitsa bwanji kuchita mautumiki amenewo ngakhale ali ndi udindo wosamalira banja? Kodi amatani kuti aziika ntchito yolalikira pamalo oyamba? Kodi banja lawo lawathandiza bwanji kuti azikwanitsa kuchita utumiki wawo?

Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena