Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 5/14 tsamba 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa May 19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa May 19
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA MAY 19
Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
km 5/14 tsamba 2

Ndandanda ya Mlungu wa May 19

MLUNGU WOYAMBIRA MAY 19

Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 11 ndime 15-21 (Mph. 30)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Ekisodo 30-33 (Mph. 10)

Na. 1: Ekisodo 32:1-14 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Malamulo Khumi Anathera Limodzi ndi Chilamulo cha Mose—rs tsa. 348 ndime 2-3 (Mph. 5)

Na. 3: N’chifukwa Chiyani Sitiyenera Kuopa Satana Ndiponso Ziwanda Zake?—bh tsa. 104-105 ndime 17-19 (Mph. 5)

Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 45

Mph. 10: Ndife Atumiki a Uthenga Wabwino. Nkhani yolimbikitsa yochokera m’buku la Gulu, tsamba 77 mpaka 78 ndime 2. Pemphani omvera kuti afotokoze chimene chimachititsa kuti azisangalala ndi utumiki.

Mph. 10: Kodi Mungachite Upainiya Wothandiza pa Nthawi ya Holide? Nkhani yokambirana. Pogwiritsa ntchito ndime 1 patsamba 113 m’buku la Gulu, fotokozani mwachidule zofunika kuti munthu akhale mpainiya wothandiza. Pemphani amene anachita upainiya wothandiza pa holide ya kusukulu kapena kuntchito kuti afotokoze madalitso amene anapeza. Limbikitsani onse kuti aganizire ngati angakwanitse kudzachita upainiya pa nthawi ya holide.

Mph. 10: “Yesetsani Kuti Muzisunga Nthawi.” Mafunso ndi mayankho. Mukamakambirana ndime 4, pemphani omvera kuti afotokoze zimene zimawathandiza kuti azisunga nthawi.

Nyimbo Na. 44 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena