Zochitika mu Utumiki Wakumunda
M’mwezi wa January chaka chino, abale ndi alongo okwana 2,744 anachita upainiya wothandiza. N’zodziwikiratu kuti Yehova sadzaiwala khama lawo ndipo adzadalitsa onse amene akudzipereka kugwira ntchito yofunika kwambiri imeneyi.—Aheb. 6:10.